Yesaya 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 41:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzachititsa kuti mitsinje yamadzi iyende mʼmapiri opanda zomera zilizonse+Komanso kuti akasupe atuluke mʼzigwa.+ Chipululu ndidzachisandutsa dambo lamadziNdipo dziko lopanda madzi ndidzalisandutsa akasupe amadzi.+ Yesaya 58:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
18 Ndidzachititsa kuti mitsinje yamadzi iyende mʼmapiri opanda zomera zilizonse+Komanso kuti akasupe atuluke mʼzigwa.+ Chipululu ndidzachisandutsa dambo lamadziNdipo dziko lopanda madzi ndidzalisandutsa akasupe amadzi.+