1 Mafumu 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zinali choncho chifukwa mfumuyo inali ndi zombo za ku Tarisi+ zomwe zinkayenda panyanja pamodzi ndi zombo za Hiramu. Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombozo zinkabweretsa golide, siliva, minyanga ya njovu,+ anyani ndi mbalame zotchedwa pikoko. Ezekieli 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Sitima zapamadzi za ku Tarisi+ zinkanyamula katundu wako wamalonda,Choncho unali ndi chuma chambiri ndipo unalemera* pakati pa nyanja.
22 Zinali choncho chifukwa mfumuyo inali ndi zombo za ku Tarisi+ zomwe zinkayenda panyanja pamodzi ndi zombo za Hiramu. Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombozo zinkabweretsa golide, siliva, minyanga ya njovu,+ anyani ndi mbalame zotchedwa pikoko.
25 Sitima zapamadzi za ku Tarisi+ zinkanyamula katundu wako wamalonda,Choncho unali ndi chuma chambiri ndipo unalemera* pakati pa nyanja.