Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 30:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Siliva amene munakutira mafano anu ogoba komanso golide amene munakutira mafano anu achitsulo,*+ mudzamuchititsa kuti akhale wonyansa. Mudzamutaya ngati mmene mkazi amene akusamba amatayira kansalu kake, ndipo mudzanena kuti: “Nyansi zimenezi!”+

  • Yesaya 31:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chifukwa pa tsiku limenelo, aliyense wa inu adzataya milungu yake yasiliva yomwe ndi yachabechabe komanso milungu yake yagolide yopanda phindu, imene manja anu anapanga nʼkukuchimwitsani.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani