-
Yesaya 41:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Choncho mmisiri wa mitengo akulimbikitsa mmisiri wa zitsulo.+
Amene amawongola zitsulo ndi hamala
Akulimbikitsa munthu amene akusula zitsulo ndi hamala.
Ponena za ntchito yowotcherera zitsulo ndi mtovu, iye akuti: “Zili bwino.”
Kenako amakhomerera fanolo ndi misomali kuti lisagwe.
-
-
Yeremiya 10:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Miyambo ya anthu amenewa ndi yopanda pake.
-