-
Mlaliki 8:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ngakhale woipa atachita zoipa maulendo 100 nʼkukhalabe ndi moyo wautali, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino, chifukwa chakuti amamuopa.+
-