Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 87:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Iwe mzinda wa Mulungu woona, anthu akunena za ulemerero wako.+ (Selah)

  • Ezekieli 43:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iye anandiuza kuti:

      “Iwe mwana wa munthu, awa ndi malo a mpando wanga wachifumu+ ndiponso poikapo mapazi anga.+ Ndidzakhala pamalo amenewa, pakati pa Aisiraeli mpaka kalekale.+ Nyumba ya Isiraeli ndi mafumu awo sadzaipitsanso dzina langa loyera+ pochita uhule ndi milungu ina komanso ndi mitembo ya mafumu awo.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani