-
Yeremiya 36:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Komanso mfumu inalamula Yerameeli mwana wa mfumu, Seraya mwana wa Azirieli ndi Selemiya mwana wa Abideeli kuti akagwire Baruki mlembi ndi mneneri Yeremiya, koma Yehova anawabisa.+
-