-
2 Mafumu 25:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ena mwa anthu osauka kwambiri amʼdzikolo, mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anawasiya kuti akhale olima minda ya mpesa ndi alimi ogwira ntchito mokakamizidwa.+
-
-
Yeremiya 52:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ena mwa anthu osauka kwambiri amʼdzikolo, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anawasiya kuti akhale olima minda ya mpesa ndi anthu ogwira ntchito mokakamizidwa.+
-