Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Mafumu 25:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno Nebukadinezara mfumu ya Babulo, anasankha Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani,+ kuti akhale mtsogoleri wa anthu amene anawasiya ku Yuda.+

  • Yeremiya 40:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Yeremiya akuganizira koti apite, Nebuzaradani anamuuza kuti: “Bwerera kwa Gedaliya,+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ amene mfumu ya Babulo yamuika kuti azilamulira mizinda ya Yuda. Ukakhale naye pakati pa anthuwo, kapena ukhoza kupita kulikonse kumene ungakonde.”

      Kenako mkulu wa asilikali olondera mfumu anamupatsa chakudya chapaulendo ndi mphatso ndipo anamulola kuti apite.

  • Yeremiya 41:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Isimaeli mwana wa Netaniya ndi amuna 10 amene anali naye ananyamuka nʼkupha ndi lupanga Gedaliya mwana wa Ahikamu, mwana wa Safani. Choncho Isimaeli anapha munthu amene mfumu ya Babulo inamuika kuti azilamulira dzikolo.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani