Maliro 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wasonyeza ukali wake.Wakhuthula mkwiyo wake woyaka moto.+ Ndipo iye wayatsa moto mʼZiyoni, umene wawotcha maziko ake.+
11 Yehova wasonyeza ukali wake.Wakhuthula mkwiyo wake woyaka moto.+ Ndipo iye wayatsa moto mʼZiyoni, umene wawotcha maziko ake.+