Deuteronomo 32:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamvera chisoni atumiki ake+Akadzaona kuti mphamvu zawo zatha,Komanso kuti kwangotsala anthu ovutika ndi ofooka. Yeremiya 18:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nthawi iliyonse imene ndinganene kuti ndizula, kugwetsa ndi kuwononga mtundu uliwonse wa anthu kapena ufumu,+ 8 ndiyeno mtundu wa anthuwo nʼkusiya zoipa zimene ndinawadzudzula nazo, inenso ndidzasintha maganizo anga okhudza tsoka limene ndimafuna kuwagwetsera.+ Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamvera chisoni atumiki ake+Akadzaona kuti mphamvu zawo zatha,Komanso kuti kwangotsala anthu ovutika ndi ofooka.
7 Nthawi iliyonse imene ndinganene kuti ndizula, kugwetsa ndi kuwononga mtundu uliwonse wa anthu kapena ufumu,+ 8 ndiyeno mtundu wa anthuwo nʼkusiya zoipa zimene ndinawadzudzula nazo, inenso ndidzasintha maganizo anga okhudza tsoka limene ndimafuna kuwagwetsera.+