-
Numeri 21:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Tsoka iwe Mowabu! Mudzawonongedwa, inu anthu a Kemosi!+
Iye adzapangitsa ana ake aamuna kukhala othawa kwawo, ndipo adzasandutsa ana ake aakazi kukhala akapolo a Sihoni, mfumu ya Aamori.
-