-
Yeremiya 48:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 “Tamva za kunyada kwa Mowabu. Iye ndi wodzikuza kwambiri.
Tamva za kudzitukumula kwake, kunyada kwake, kudzikweza kwake ndi kudzikuza kwa mtima wake.”+
-