Yeremiya 51:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Babulo wagwa mwadzidzidzi ndipo wasweka.+ Mulirireni mofuula.+ Mʼpatseni mafuta a basamu kuti ululu wake uthe, mwina angachire.” Chivumbulutso 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
8 Babulo wagwa mwadzidzidzi ndipo wasweka.+ Mulirireni mofuula.+ Mʼpatseni mafuta a basamu kuti ululu wake uthe, mwina angachire.”