Mika 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Weta anthu ako ndi ndodo yako, gulu la nkhosa zomwe ndi cholowa chako,+Zimene zinkakhala zokhazokha mʼnkhalango komanso pakati pa mitengo ya zipatso. Uzilole zikadyere ku Basana ndi ku Giliyadi+ ngati mmene zinkachitira kale.
14 Weta anthu ako ndi ndodo yako, gulu la nkhosa zomwe ndi cholowa chako,+Zimene zinkakhala zokhazokha mʼnkhalango komanso pakati pa mitengo ya zipatso. Uzilole zikadyere ku Basana ndi ku Giliyadi+ ngati mmene zinkachitira kale.