-
Yeremiya 51:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Munthu amene watumidwa kukanena uthenga wakumana ndi mnzake,
Ndipo mthenga wina wakumana ndi mnzake.
Onsewa akukanena kwa mfumu ya Babulo kuti mzinda wake walandidwa kumbali zonse.+
-
Danieli 5:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Usiku womwewo, Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa.+
-
-
-