Yesaya 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo akubwera kuchokera kudziko lakutali,+Kuchokera kumalo akutali kwambiri pansi pa thambo,Yehova akubwera ndi zida zamkwiyo wake,Kuti awononge dziko lonse lapansi.+ Yeremiya 51:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake.
5 Iwo akubwera kuchokera kudziko lakutali,+Kuchokera kumalo akutali kwambiri pansi pa thambo,Yehova akubwera ndi zida zamkwiyo wake,Kuti awononge dziko lonse lapansi.+
11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake.