Yesaya 45:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndidzakupatsa chuma chimene chili mumdimaNdiponso chuma chimene chabisidwa mʼmalo achinsinsi,+Kuti udziwe kuti ine ndine Yehova,Mulungu wa Isiraeli, amene ndikukuitana pokutchula dzina lako.+ Yeremiya 50:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Lupanga lidzawononga mahatchi awo, magaleta awo ankhondoNdi anthu onse a mitundu yosiyanasiyana amene ali pakati pawoNdipo adzakhala ngati akazi.+ Lupanga lidzawononga chuma chake ndipo anthu ena adzachitenga.+
3 Ndidzakupatsa chuma chimene chili mumdimaNdiponso chuma chimene chabisidwa mʼmalo achinsinsi,+Kuti udziwe kuti ine ndine Yehova,Mulungu wa Isiraeli, amene ndikukuitana pokutchula dzina lako.+
37 Lupanga lidzawononga mahatchi awo, magaleta awo ankhondoNdi anthu onse a mitundu yosiyanasiyana amene ali pakati pawoNdipo adzakhala ngati akazi.+ Lupanga lidzawononga chuma chake ndipo anthu ena adzachitenga.+