Yeremiya 50:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova, mʼdzikomo simudzakhalanso anthu.+Dziko lonselo lidzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi Babulo adzayangʼanitsitsa mwamanthaNdipo adzamuimbira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+ Yeremiya 50:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Mofanana ndi mmene Mulungu anawonongera Sodomu ndi Gomora+ komanso midzi imene anali nayo pafupi,+ ndi mmenenso zidzakhalire ndi Babulo. Palibe aliyense amene adzakhalenso mumzindawo,”+ akutero Yehova. Chivumbulutso 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
13 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova, mʼdzikomo simudzakhalanso anthu.+Dziko lonselo lidzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi Babulo adzayangʼanitsitsa mwamanthaNdipo adzamuimbira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+
40 “Mofanana ndi mmene Mulungu anawonongera Sodomu ndi Gomora+ komanso midzi imene anali nayo pafupi,+ ndi mmenenso zidzakhalire ndi Babulo. Palibe aliyense amene adzakhalenso mumzindawo,”+ akutero Yehova.