Yeremiya 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwana,+ ndidzalanga mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo chifukwa cha zolakwa zawo.+ Ndipo dziko la Akasidi ndidzalisandutsa bwinja mpaka kalekale,’ akutero Yehova.+ Yeremiya 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mufuulireni mfuu yankhondo kuchokera kumbali zonse. Iye wavomereza kuti wagonja.* Zipilala zake zagwa, mipanda yake yagwetsedwa,+Chifukwa Yehova akumubwezera.+ Inunso mubwezereni. Muchitireni zimene iye anakuchitirani.+
12 ‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwana,+ ndidzalanga mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo chifukwa cha zolakwa zawo.+ Ndipo dziko la Akasidi ndidzalisandutsa bwinja mpaka kalekale,’ akutero Yehova.+
15 Mufuulireni mfuu yankhondo kuchokera kumbali zonse. Iye wavomereza kuti wagonja.* Zipilala zake zagwa, mipanda yake yagwetsedwa,+Chifukwa Yehova akumubwezera.+ Inunso mubwezereni. Muchitireni zimene iye anakuchitirani.+