Yeremiya 50:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mʼdzikomo mukumveka phokoso lankhondo,Tsoka lalikulu lawagwera. 23 Taonani! Hamala yophwanyira mitundu ya anthu padziko lonse lapansi yathyoledwa nʼkuwonongedwa.+ Taonani! Babulo wakhala chinthu chochititsa mantha pakati pa anthu a mitundu ina.+
22 Mʼdzikomo mukumveka phokoso lankhondo,Tsoka lalikulu lawagwera. 23 Taonani! Hamala yophwanyira mitundu ya anthu padziko lonse lapansi yathyoledwa nʼkuwonongedwa.+ Taonani! Babulo wakhala chinthu chochititsa mantha pakati pa anthu a mitundu ina.+