-
Yesaya 59:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Tikungopapasa khoma ngati anthu amene ali ndi vuto losaona,
Tikungopapasapapasa ngati anthu opanda maso.+
Tikupunthwa masanasana ngati kuti tili mumdima wamadzulo.
Pakati pa anthu amphamvu tikungokhala ngati anthu akufa.
-