-
Yeremiya 30:12, 13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Yehova wanena kuti:
“Kuwonongeka kwako ndi kosachiritsika.+
Ndiponso bala lako ndi losachiritsika.
13 Palibe woti akuchonderere pa mlandu wako.
Palibe njira iliyonse yochiritsira bala lako.
Ndipo palibe mankhwala amene angakuchiritse.
-