-
Yeremiya 6:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Choncho Yehova wanena kuti:
“Tsopano ndikuikira anthu awa zinthu zopunthwitsa,
Ndipo iwo adzapunthwa ndi zinthu zimenezi,
Abambo limodzi ndi ana,
Munthu ndi mnzake woyandikana naye,
Onse adzawonongedwa.”+
-