-
Yeremiya 8:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Chisoni changa nʼchosachiritsika.
Mtima wanga ukudwala.
-
-
Yeremiya 8:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndasweka mtima chifukwa cha kuwonongeka kwa mwana wamkazi wa anthu anga.+
Ndine wachisoni.
Ndipo ndili ndi mantha aakulu.
-
-
Yeremiya 9:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndikanakonda mʼmutu mwanga mukanakhala madzi ambiri,
Ndiponso maso anga akanakhala kasupe wa misozi.+
Zikanatero, ndikanalira masana ndi usiku
Chifukwa cha anthu a mtundu wanga amene aphedwa.
-