-
Yeremiya 52:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga ena mwa anthu onyozeka ndiponso anthu ena onse amene anatsala mumzindawo. Anatenganso anthu amene anathawira kwa mfumu ya Babulo komanso amisiri onse aluso nʼkupita nawo ku ukapolo.+
-