Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 29:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Chifukwa chakuti watumiza makalata mʼdzina lako kwa anthu onse amene ali ku Yerusalemu, kwa Zefaniya+ mwana wa Maaseya, amene ndi wansembe ndi kwa ansembe onse, onena kuti,

  • Yeremiya 37:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inatuma Yehukali+ mwana wa Selemiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya wansembe kwa mneneri Yeremiya kukamuuza kuti: “Chonde, tipempherere kwa Yehova Mulungu wathu.”

  • Yeremiya 52:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri ndi alonda atatu apakhomo.+

  • Yeremiya 52:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo ku Ribila+ mʼdziko la Hamati. Choncho Ayuda anatengedwa kudziko lawo nʼkupita nawo ku ukapolo.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani