Levitiko 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye waikira chizindikiro mtundu wakutali.+Wauimbira likhweru kuti ubwere kuchokera kumapeto kwa dziko lapansi.+Ndipotu mtunduwo ukubwera mofulumira kwambiri.+ Yeremiya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova wanena kuti, ‘Ndikuitana mafuko onse a maufumu a kumpoto.+Iwo adzabwera ndipo aliyense adzakhazikitsa mpando wake wachifumu,Pakhomo la mageti a Yerusalemu.+Iwo adzaukira mpanda wake wonseNdi mizinda yonse ya Yuda.+
26 Iye waikira chizindikiro mtundu wakutali.+Wauimbira likhweru kuti ubwere kuchokera kumapeto kwa dziko lapansi.+Ndipotu mtunduwo ukubwera mofulumira kwambiri.+
15 Yehova wanena kuti, ‘Ndikuitana mafuko onse a maufumu a kumpoto.+Iwo adzabwera ndipo aliyense adzakhazikitsa mpando wake wachifumu,Pakhomo la mageti a Yerusalemu.+Iwo adzaukira mpanda wake wonseNdi mizinda yonse ya Yuda.+