-
Yesaya 63:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndinapondaponda mitundu ya anthu nditakwiya,
Ndinawaledzeretsa ndi ukali wanga.+
Ndipo magazi awo ndinawathira pansi.”
-