-
Yeremiya 18:19, 20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndimvereni, inu Yehova,
Ndipo imvani zimene adani anga akunena.
20 Kodi akuyenera kubwezera zinthu zoipa pa zinthu zabwino?
Iwo akumba dzenje kuti achotse moyo wanga.+
Kumbukirani kuti ndinkaima pamaso panu nʼkumalankhula zabwino zokhudza anthu amenewa,
Kuti muwachotsere mkwiyo wanu.
-