Yeremiya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Koma iwe ukonzekere kugwira ntchito,*Ndipo upite ukawauze zonse zimene ndakulamula. Usachite nawo mantha,+Kuti ndisakupangitse kuchita nawo mantha kwambiri.
17 “Koma iwe ukonzekere kugwira ntchito,*Ndipo upite ukawauze zonse zimene ndakulamula. Usachite nawo mantha,+Kuti ndisakupangitse kuchita nawo mantha kwambiri.