-
2 Mafumu 22:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Safani mlembi anauzanso mfumuyo kuti: “Wansembe Hilikiya wandipatsa buku+ linalake.” Ndiyeno Safani anayamba kuwerengera mfumu bukulo.
-