Yeremiya 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwana,+ ndidzalanga mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo chifukwa cha zolakwa zawo.+ Ndipo dziko la Akasidi ndidzalisandutsa bwinja mpaka kalekale,’ akutero Yehova.+ Yeremiya 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa mitundu yambiri ndi mafumu otchuka+ adzawagwiritsa ntchito ngati akapolo+ ndipo ndidzawabwezera mogwirizana ndi zochita zawo komanso ntchito ya manja awo.’”+ Yeremiya 51:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake.
12 ‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwana,+ ndidzalanga mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo chifukwa cha zolakwa zawo.+ Ndipo dziko la Akasidi ndidzalisandutsa bwinja mpaka kalekale,’ akutero Yehova.+
14 Chifukwa mitundu yambiri ndi mafumu otchuka+ adzawagwiritsa ntchito ngati akapolo+ ndipo ndidzawabwezera mogwirizana ndi zochita zawo komanso ntchito ya manja awo.’”+
11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake.