Yesaya 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yeremiya 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwana,+ ndidzalanga mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo chifukwa cha zolakwa zawo.+ Ndipo dziko la Akasidi ndidzalisandutsa bwinja mpaka kalekale,’ akutero Yehova.+
12 ‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwana,+ ndidzalanga mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo chifukwa cha zolakwa zawo.+ Ndipo dziko la Akasidi ndidzalisandutsa bwinja mpaka kalekale,’ akutero Yehova.+