Yeremiya 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pachifukwa chimenechi dzikolo lidzalira,+Ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndasankha kuchita zimenezi,Ndipo sindidzasintha maganizo anga* kapena kulephera kuchita zimenezi.+
28 Pachifukwa chimenechi dzikolo lidzalira,+Ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndasankha kuchita zimenezi,Ndipo sindidzasintha maganizo anga* kapena kulephera kuchita zimenezi.+