-
Yeremiya 4:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Popeza tsopano wawonongedwa, ndiye utani?
Unkakonda kuvala zovala zamtengo wapatali,*
Kudzikongoletsa ndi zokongoletsera zagolide
Ndiponso kukongoletsa mʼmaso mwako ndi penti wakuda.
-
-
Ezekieli 16:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 ine ndikusonkhanitsa pamodzi zibwenzi zako zonse zimene unkazisangalatsa, onse amene unkawakonda limodzi ndi onse amene unkadana nawo. Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumadera onse ozungulira kuti akuukire ndipo ndidzakuvula kuti aone maliseche ako, moti adzakuona uli mbulanda.+
-