Ezekieli 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, yangʼana Gogi wa kudziko la Magogi,+ mtsogoleri wamkulu* wa Meseki ndi Tubala+ ndipo ulosere zoipa zimene zidzamuchitikire.+
2 “Iwe mwana wa munthu, yangʼana Gogi wa kudziko la Magogi,+ mtsogoleri wamkulu* wa Meseki ndi Tubala+ ndipo ulosere zoipa zimene zidzamuchitikire.+