Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mafumu 6:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Chipinda chamkaticho chinali mikono 20 mulitali, mikono 20 mulifupi ndi mikono 20 kupita mʼmwamba.+ Chipindachi anachikuta ndi golide woyenga bwino, komanso anakuta guwa lansembe+ ndi matabwa a mkungudza.

  • 2 Mbiri 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kenako iye anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ Mulitali mwake chinali mikono 20 mofanana ndi mulifupi mwa nyumbayo ndipo mulifupi mwake chinali mikono 20. Anachikuta ndi golide wabwino wokwana matalente* 600.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani