Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mafumu 6:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Makoma a mkati mwa nyumbayo anawamanga ndi matabwa akuluakulu a mkungudza. Mkati mwa nyumbayo, kuchokera pansi mpaka kudenga anakutamo ndi matabwa. Komanso pansi pa nyumbayo anaikapo matabwa akuluakulu a mitengo ya junipa.*+

  • 2 Mbiri 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Nyumba yaikuluyo anaikuta ndi matabwa a mitengo ya junipa,* kenako anaikutanso ndi golide wabwino.+ Atatero, anaikongoletsa ndi matcheni+ ndiponso zithunzi za mitengo yakanjedza zojambula mochita kugoba.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani