-
Ezekieli 40:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Kudzera mʼmasomphenya ochokera kwa Mulungu, iye ananditenga nʼkupita nane mʼdziko la Isiraeli nʼkukandikhazika paphiri lalitali kwambiri.+ Mbali yakumʼmwera paphiripo panali chinachake chooneka ngati mzinda.
-