Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ezekieli 42:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pafupi ndi malo opanda kanthu komanso nyumba imene inali kumadzulo, mkati* mwa mpanda wamiyala wa bwalo, kumbali yakumʼmawa, kunalinso nyumba zodyera.+ 11 Pakati pa nyumba zodyerazo panali njira yofanana ndi ya nyumba zodyera za mbali yakumpoto.+ Mulitali ndi mulifupi mwa nyumbazo, makomo otulukira komanso kamangidwe kake zinali zofanana ndi za nyumba za kumpoto zija. Makomo ake olowera

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani