Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ezekieli 41:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kumadzulo kwa kachisi kunalinso nyumba ina imene inayangʼanizana ndi malo opanda kanthu. Nyumbayi inali mikono 70 mulifupi ndipo mulitali mwake inali mikono 90. Khoma la nyumbayo linali lochindikala mikono 5, kuzungulira nyumba yonseyo.

  • Ezekieli 42:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Kenako munthu uja anandipititsa kubwalo lakunja mbali yakumpoto.+ Ndiyeno anandipititsa kunyumba imene inali ndi zipinda zodyera yomwe inali pafupi ndi malo opanda kanthu,+ kumpoto kwa nyumba imene inali kumadzulo.*+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani