Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Levitiko 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano lamulo la nsembe yambewu+ ndi ili: Ana a Aroni azibweretsa nsembeyi pamaso pa Yehova patsogolo pa guwa lansembe.

  • Levitiko 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Aroni ndi ana ake azidya zotsala za nsembe imeneyi.+ Azipanga mkate wopanda zofufumitsa ndi kudya mkatewo mʼmalo oyera. Aziudyera mʼbwalo la chihema chokumanako.+

  • Levitiko 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “‘Lamulo la nsembe yakupalamula+ ndi ili: Nsembeyi ndi yopatulika koposa.

  • Levitiko 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mwamuna aliyense yemwe ndi wansembe azidya nyamayo+ ndipo aziidyera mʼmalo oyera. Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+

  • Levitiko 10:12, 13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiyeno Mose analankhula ndi Aroni komanso Eleazara ndi Itamara, ana a Aroni amene anatsala kuti: “Tengani nsembe yambewu imene yatsala pa nsembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova, ndipo muidye yopanda zofufumitsa pafupi ndi guwa lansembe,+ chifukwa nsembeyo ndi yopatulika koposa.+ 13 Mudye nsembeyo mʼmalo oyera,+ chifukwa ndi gawo lanu komanso ndi gawo la ana anu kuchokera pa nsembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova. Zimenezi nʼzimene ndalamulidwa.

  • Levitiko 24:8, 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Numeri 18:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Uzilidyera mʼmalo oyera koposa,+ ndipo mwamuna aliyense wa fuko lanu angathe kudya nawo. Gawo limenelo lizikhala chinthu chopatulika kwa iwe.+

  • Ezekieli 40:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Chipinda chodyeramo chimene chayangʼana kumpoto ndi cha ansembe amene amagwira ntchito zokhudza utumiki wapaguwa lansembe,+ omwe ndi ana a Zadoki.+ Amenewa ndi Alevi amene anapatsidwa udindo woti azifika pamaso pa Yehova nʼkumamutumikira.”+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani