Levitiko 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo zotsala pa nsembe yambewu zizikhala za Aroni ndi ana ake,+ chifukwa ndi zopatulika koposa,+ zochokera pansembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova. Numeri 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Nehemiya 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
3 Ndipo zotsala pa nsembe yambewu zizikhala za Aroni ndi ana ake,+ chifukwa ndi zopatulika koposa,+ zochokera pansembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova.