-
Ezekieli 40:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Kenako anafika pageti limene linayangʼana kumʼmawa+ nʼkukwera masitepe ake. Atayeza malo apafupi ndi khomo la kanyumba kapagetiko, anapeza kuti anali bango limodzi mulifupi. Malo apafupi ndi khomo lambali ina ya kanyumbako analinso bango limodzi mulifupi mwake.
-