Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Numeri 18:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Deuteronomo 18:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Alevi omwe ndi ansembe, komanso fuko lonse la Levi, sadzapatsidwa gawo kapena cholowa pakati pa Aisiraeli. Iwo azidzadya nsembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova, zomwe ndi cholowa chake.+

  • Yoswa 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Fuko la Levi lokha ndi limene sanalipatse malo monga cholowa chawo.+ Cholowa chawo ndi nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ mogwirizana ndi zimene anawalonjeza.+

  • Ezekieli 45:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Malo amenewa adzakhale gawo lopatulika la ansembe mʼdzikoli,+ omwe ndi atumiki apamalo opatulika, amene amayandikira kwa Yehova nʼkumamutumikira.+ Malo amenewa adzakhala oti adzamangepo nyumba zawo komanso adzakhala malo opatulika omangapo kachisi.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani