Yesaya 59:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukonde wawo wa kangaude sudzakhala chovala chawo,Ndipo zochita zawo sizingawathandize.+ Ntchito zawo nʼzopweteka ena,Ndipo mʼmanja mwawo muli ntchito zachiwawa.+ Mika 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amalakalaka minda ya anthu ena ndipo amaitenga.+Amalakalakanso nyumba za anthu ena nʼkuzitenga.Amatenga mwachinyengo nyumba ya munthu,+Ndipo amatenganso cholowa cha munthu.
6 Ukonde wawo wa kangaude sudzakhala chovala chawo,Ndipo zochita zawo sizingawathandize.+ Ntchito zawo nʼzopweteka ena,Ndipo mʼmanja mwawo muli ntchito zachiwawa.+
2 Iwo amalakalaka minda ya anthu ena ndipo amaitenga.+Amalakalakanso nyumba za anthu ena nʼkuzitenga.Amatenga mwachinyengo nyumba ya munthu,+Ndipo amatenganso cholowa cha munthu.