-
Ezekieli 11:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Nditangomaliza kulosera, Pelatiya mwana wa Benaya anamwalira. Choncho ine ndinagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yanga pansi, nʼkufuula kuti: “Mayo ine, inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Kodi mukufuna kuwononga Aisiraeli amene atsalawa?”+
-