Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti:

      “Dulani mitengo kuti timange malo okwera oti timenyerepo nkhondo* ndi Yerusalemu.+

      Yerusalemu ndi mzinda umene ukuyenera kuimbidwa mlandu.

      Mkati mwake muli kuponderezana kokhakokha.+

  • Yeremiya 32:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Taonani! Anthu abwera kumzinda uno ndipo amanga malo okwera omenyerapo nkhondo kuti aulande,+ moti uperekedwa mʼmanja mwa Akasidi amene akumenyana ndi anthu amumzindawu. Anthu adzafa ndi lupanga,+ njala ndi mliri.*+ Zinthu zonse zimene munanena zachitika ndipo ndi izi mukuzionazi.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani