-
Ezekieli 12:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Unyamule katunduyo paphewa iwo akuona ndipo umutulutse kuli mdima. Uphimbe nkhope yako kuti usaone pansi chifukwa ndakuika kuti ukhale chizindikiro ku mtundu wa Isiraeli.”+
-
-
Ezekieli 24:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ezekieli wakhala chizindikiro kwa inu.+ Mudzachita zonse zimene iye wachita. Tsokali likadzakugwerani, mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”’”
-